Kupanga apply jokes kupangila chiwaliwali koma abale kkkkkkk
@hamzamabvuto692014 годин тому
Top fan for Mr jokes watching from South Africa timapempha kt ma episode akumafupika please Bola atamafikako 25 or 30 minutes please Mr jokes ine wanu top fan from South Africa Johannesburg mbite
@wakatbilly893314 годин тому
😂😂😂😂😂😂😂Apa ndie yalakwa jokes
@FranciscosimaoSimaoJon-kt5vp14 годин тому
Mbambande jokes umakwana
@NgomaRaheem14 годин тому
Kma jokes😂😂😂😂😂
@iscolinyasa957514 годин тому
Kwayipha 😂😂 Now Thoko vs Jokes
@user-sk1wj9bw6l14 годин тому
Kkkkkkkk ilibwinotu iyi tikudikira kut what a next
@victorbanda903915 годин тому
Jokes ufiti
@user-yx3mz4so2s15 годин тому
Kkkkkk next episode kuvuta😂😂😂
@wahosonsoso15 годин тому
Eee kwachema ndi tu
@Blemlima15 годин тому
Kkk zakumanaso joke + thoko, ee kwachema
@medsonwalaza881315 годин тому
Mwana ovuta kulera
@medsonwalaza881315 годин тому
Next please.... Mukumatenga zaka zitatu kuti muponye ina... Komaso ma episode ndikuwona ngati akumafupika... Nde timati mutiganizireko mwina afike pa 25 kapena 30 minutes.... Ndatha ine wanu "TOP FAN"